MARANATHA YAFIKA KU LILONGWE
- Sukulu yanu yotchuka ija ya Maranatha yatsekula nthambi yake ku Lilongwe
- Pafupi ndi Round about ya nsewu wa Bunda Bypass apa ndi pa 6 Miles.
- Pitani ndi mwana wanu mtsikana mulembetse.
- Mukafuna kumva zambiri imbani kwa a Principal pa #0991276273.
- SUKULU ATSEKULIRA PA 11 SEPTEMBER 2023